Ekisodo 8:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Zitatero Mose anachoka pamaso pa Farao ndipo anapita kukachonderera Yehova.+