Ekisodo 9:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ndiyeno Mose anachoka pamaso pa Farao, n’kutuluka mumzindawo. Kenako anakweza manja ake kwa Yehova, ndipo mabingu ndi matalala zinasiya, mvulanso inasiya kugwa padziko lapansi.+ Yakobo 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho muululirane machimo anu poyera+ ndi kupemphererana, kuti muchiritsidwe.+ Pembedzero la munthu wolungama limagwira ntchito mwamphamvu kwambiri.+
33 Ndiyeno Mose anachoka pamaso pa Farao, n’kutuluka mumzindawo. Kenako anakweza manja ake kwa Yehova, ndipo mabingu ndi matalala zinasiya, mvulanso inasiya kugwa padziko lapansi.+
16 Choncho muululirane machimo anu poyera+ ndi kupemphererana, kuti muchiritsidwe.+ Pembedzero la munthu wolungama limagwira ntchito mwamphamvu kwambiri.+