Salimo 135:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Anasonyeza zizindikiro ndi kuchita zozizwitsa pakati pako Iguputo iwe,+Anachita zimenezo kwa Farao ndi kwa atumiki ake onse.+
9 Anasonyeza zizindikiro ndi kuchita zozizwitsa pakati pako Iguputo iwe,+Anachita zimenezo kwa Farao ndi kwa atumiki ake onse.+