Numeri 33:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pambuyo pake ananyamuka ku Pihahiroti, n’kukadutsa panyanja+ kuwolokera kuchipululu.+ Anayendabe ulendo wa masiku atatu m’chipululu cha Etamu,+ n’kukamanga msasa ku Mara.+
8 Pambuyo pake ananyamuka ku Pihahiroti, n’kukadutsa panyanja+ kuwolokera kuchipululu.+ Anayendabe ulendo wa masiku atatu m’chipululu cha Etamu,+ n’kukamanga msasa ku Mara.+