Numeri 33:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako ananyamuka ku Mara n’kukafika ku Elimu.+ Ku Elimuko anapezako akasupe 12 a madzi, ndi mitengo 70 ya kanjedza, ndipo anamanga msasa kumeneko.
9 Kenako ananyamuka ku Mara n’kukafika ku Elimu.+ Ku Elimuko anapezako akasupe 12 a madzi, ndi mitengo 70 ya kanjedza, ndipo anamanga msasa kumeneko.