Ekisodo 15:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kenako anafika ku Elimu, kumene kunali akasupe 12 a madzi ndi mitengo 70 ya kanjedza.+ Iwo anamanga msasa pamenepo pafupi ndi madzi.
27 Kenako anafika ku Elimu, kumene kunali akasupe 12 a madzi ndi mitengo 70 ya kanjedza.+ Iwo anamanga msasa pamenepo pafupi ndi madzi.