Machitidwe 7:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Atamva mawu amenewa, Mose anathawa ndi kukakhala kuchilendo m’dziko la Midiyani.+ Kumeneko anabereka ana aamuna awiri.+
29 Atamva mawu amenewa, Mose anathawa ndi kukakhala kuchilendo m’dziko la Midiyani.+ Kumeneko anabereka ana aamuna awiri.+