Aheberi 12:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Simunafike paphiri limene panamveka kulira kwa lipenga+ ndi mawu a winawake akulankhula,+ amene anthu atawamva, anachonderera kuti asawauzenso mawu ena.+
19 Simunafike paphiri limene panamveka kulira kwa lipenga+ ndi mawu a winawake akulankhula,+ amene anthu atawamva, anachonderera kuti asawauzenso mawu ena.+