Ekisodo 23:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Samala ndipo umvere mawu ake. Usam’pandukire, chifukwa sadzalekerera zolakwa zanu,+ pakuti dzina langa lili mwa iye.
21 Samala ndipo umvere mawu ake. Usam’pandukire, chifukwa sadzalekerera zolakwa zanu,+ pakuti dzina langa lili mwa iye.