Salimo 37:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Munthu woipa amakongola zinthu za ena koma osabweza,+Koma wolungama amakomera mtima ena ndipo amapereka mphatso.+ Miyambo 22:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Wolemera ndi amene amalamulira anthu osauka,+ ndipo wobwereka amakhala kapolo wa wobwereketsayo.+
21 Munthu woipa amakongola zinthu za ena koma osabweza,+Koma wolungama amakomera mtima ena ndipo amapereka mphatso.+