Yakobo 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma inu simulemekeza munthu wosauka. Kodi si olemera amene amakusautsani+ ndi kukukokerani kumabwalo amilandu?+
6 Koma inu simulemekeza munthu wosauka. Kodi si olemera amene amakusautsani+ ndi kukukokerani kumabwalo amilandu?+