Machitidwe 18:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsopano pamene Galiyo anali bwanamkubwa+ wa Akaya, Ayuda ananyamuka mogwirizana ndi kuukira Paulo, ndipo anamutengera kumpando woweruzira milandu.+
12 Tsopano pamene Galiyo anali bwanamkubwa+ wa Akaya, Ayuda ananyamuka mogwirizana ndi kuukira Paulo, ndipo anamutengera kumpando woweruzira milandu.+