-
Machitidwe 13:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Iyeyu anali limodzi ndi bwanamkubwa Serigio Paulo, munthu wanzeru. Bwanamkubwayu anaitana Baranaba ndi Saulo, chifukwa anali kufunitsitsa kumva mawu a Mulungu.
-