Machitidwe 17:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Koma anthu ena anakhala kumbali yake ndipo anakhala otsatira a Yesu. Ena mwa iwo anali Diyonisiyo, woweruza m’bwalo la Areopagi,+ mayi wina dzina lake Damarisi ndi ena ambiri.
34 Koma anthu ena anakhala kumbali yake ndipo anakhala otsatira a Yesu. Ena mwa iwo anali Diyonisiyo, woweruza m’bwalo la Areopagi,+ mayi wina dzina lake Damarisi ndi ena ambiri.