Deuteronomo 22:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 mwamunayo azipereka masekeli 50 asiliva kwa bambo a mtsikanayo,+ ndipo akhale mkazi wake chifukwa chakuti wamunyazitsa. Sadzaloledwa kumusiya ukwati masiku onse a moyo wake.+
29 mwamunayo azipereka masekeli 50 asiliva kwa bambo a mtsikanayo,+ ndipo akhale mkazi wake chifukwa chakuti wamunyazitsa. Sadzaloledwa kumusiya ukwati masiku onse a moyo wake.+