Levitiko 22:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 “Ng’ombe, nkhosa kapena mbuzi ikabadwa, izikhala ndi mayi ake masiku 7,+ koma kuyambira tsiku la 8 kupita m’tsogolo mungaipereke kwa Yehova monga nsembe yotentha ndi moto, ndipo Mulungu adzailandira.
27 “Ng’ombe, nkhosa kapena mbuzi ikabadwa, izikhala ndi mayi ake masiku 7,+ koma kuyambira tsiku la 8 kupita m’tsogolo mungaipereke kwa Yehova monga nsembe yotentha ndi moto, ndipo Mulungu adzailandira.