Salimo 30:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Imbani nyimbo zotamanda Yehova, inu okhulupirika ake,+Yamikani dzina lake loyera.*+ Salimo 102:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma inu Yehova, mudzakhalapobe kwamuyaya,+Dzina lanu* lidzakhalapobe ku mibadwomibadwo.+ Hoseya 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iye ndi Yehova Mulungu wa makamu.+ Yehova ndilo dzina lake lomukumbukira nalo.+
4 Imbani nyimbo zotamanda Yehova, inu okhulupirika ake,+Yamikani dzina lake loyera.*+ Salimo 102:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma inu Yehova, mudzakhalapobe kwamuyaya,+Dzina lanu* lidzakhalapobe ku mibadwomibadwo.+ Hoseya 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iye ndi Yehova Mulungu wa makamu.+ Yehova ndilo dzina lake lomukumbukira nalo.+