Aefeso 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndiponso kuti kudzera mwa mtengo wozunzikirapo*+ ayanjanitse+ magulu awiri a anthuwo kwa Mulungu, ndipo anthuwo akhale thupi limodzi,+ chifukwa anali atapheratu chidanicho+ kudzera mwa iye mwini. Aefeso 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 chifukwa kudzera mwa iye, magulu onse awirife+ tingathe kufikira+ Atate mwa mzimu umodzi.+
16 Ndiponso kuti kudzera mwa mtengo wozunzikirapo*+ ayanjanitse+ magulu awiri a anthuwo kwa Mulungu, ndipo anthuwo akhale thupi limodzi,+ chifukwa anali atapheratu chidanicho+ kudzera mwa iye mwini.