Levitiko 23:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pa tsiku limeneli musagwire ntchito iliyonse, chifukwa ndi tsiku lochita mwambo wophimba machimo+ anu pamaso pa Yehova Mulungu wanu. Mateyu 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Komatu munthu ndi wofunika kwambiri kuposa nkhosa.+ Choncho, n’kololeka inde kuchita chinthu chabwino pa tsiku la sabata.” Maliko 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako anawafunsa kuti: “Kodi malamulo amalola kuchita chiti pa sabata? Chabwino kapena choipa? Kupulumutsa moyo kapena kupha?”+ Koma iwo anangokhala chete.
28 Pa tsiku limeneli musagwire ntchito iliyonse, chifukwa ndi tsiku lochita mwambo wophimba machimo+ anu pamaso pa Yehova Mulungu wanu.
12 Komatu munthu ndi wofunika kwambiri kuposa nkhosa.+ Choncho, n’kololeka inde kuchita chinthu chabwino pa tsiku la sabata.”
4 Kenako anawafunsa kuti: “Kodi malamulo amalola kuchita chiti pa sabata? Chabwino kapena choipa? Kupulumutsa moyo kapena kupha?”+ Koma iwo anangokhala chete.