Mateyu 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma iye anawayankha kuti: “Ndani wa inu amene atakhala ndi nkhosa imodzi, ndiyeno nkhosayo n’kugwera m’dzenje+ tsiku la sabata, sangaigwire ndi kuitulutsa?+ Luka 14:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Atamuona, Yesu analankhula ndi odziwa Chilamulo ndi Afarisiwo kuti: “Kodi n’kololeka kuchiritsa pa sabata kapena ayi?”+
11 Koma iye anawayankha kuti: “Ndani wa inu amene atakhala ndi nkhosa imodzi, ndiyeno nkhosayo n’kugwera m’dzenje+ tsiku la sabata, sangaigwire ndi kuitulutsa?+
3 Atamuona, Yesu analankhula ndi odziwa Chilamulo ndi Afarisiwo kuti: “Kodi n’kololeka kuchiritsa pa sabata kapena ayi?”+