Ekisodo 23:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Ukapeza ng’ombe kapena bulu wa mdani wako atasochera, um’bweze ndithu kwa mwiniwake.+ Deuteronomo 22:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Ukaona bulu wa m’bale wako kapena ng’ombe yake itagwa pamsewu usailekerere. Uzim’thandiza m’bale wako mwa kuidzutsa.+ Luka 14:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno anawauza kuti: “Ndani wa inu, amene mwana wake kapena ng’ombe yake itagwera m’chitsime+ pa tsiku la sabata, sangaitulutse nthawi yomweyo?”+
4 “Ukaona bulu wa m’bale wako kapena ng’ombe yake itagwa pamsewu usailekerere. Uzim’thandiza m’bale wako mwa kuidzutsa.+
5 Ndiyeno anawauza kuti: “Ndani wa inu, amene mwana wake kapena ng’ombe yake itagwera m’chitsime+ pa tsiku la sabata, sangaitulutse nthawi yomweyo?”+