Ekisodo 25:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ulikute ndi golide woyenga bwino, ndipo upange mkombero wagolide kuzungulira tebulo lonselo.+ 1 Mafumu 7:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 M’kupita kwa nthawi, Solomo anapanga ziwiya zonse za panyumba ya Yehova, za paguwa lansembe+ lagolide, ndi za patebulo+ limene ankaikapo mkate wachionetsero. Aheberi 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pakuti panamangidwa chipinda choyamba cha chihema.+ M’chipindamo munali choikapo nyale,+ tebulo,+ ndi mitanda ya mkate woonetsedwa,+ ndipo chinali kutchedwa “Malo Oyera.”+
48 M’kupita kwa nthawi, Solomo anapanga ziwiya zonse za panyumba ya Yehova, za paguwa lansembe+ lagolide, ndi za patebulo+ limene ankaikapo mkate wachionetsero.
2 Pakuti panamangidwa chipinda choyamba cha chihema.+ M’chipindamo munali choikapo nyale,+ tebulo,+ ndi mitanda ya mkate woonetsedwa,+ ndipo chinali kutchedwa “Malo Oyera.”+