Mateyu 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pakuti Mwana wa munthu+ ndiye Mbuye wa sabata.”+ Mateyu 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Komatu munthu ndi wofunika kwambiri kuposa nkhosa.+ Choncho, n’kololeka inde kuchita chinthu chabwino pa tsiku la sabata.” Aroma 8:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 chakuti chilengedwecho+ chidzamasulidwa+ ku ukapolo wa kuvunda n’kukhala ndi ufulu waulemerero wa ana a Mulungu.
12 Komatu munthu ndi wofunika kwambiri kuposa nkhosa.+ Choncho, n’kololeka inde kuchita chinthu chabwino pa tsiku la sabata.”
21 chakuti chilengedwecho+ chidzamasulidwa+ ku ukapolo wa kuvunda n’kukhala ndi ufulu waulemerero wa ana a Mulungu.