Ekisodo 34:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Muzigwira ntchito zanu kwa masiku 6, koma pa tsiku la 7 muzisunga sabata.+ M’nyengo yolima ndi m’nyengo yokolola muzisunga sabata.+ Levitiko 25:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma m’chaka cha 7 dzikolo lizisunga sabata lopuma pa zonse,+ sabata la Yehova. Musalime minda yanu, ndipo musatengulire mitengo yanu ya mpesa. Levitiko 25:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chaka cha 50 chizikhala chopatulika, ndipo muzilengeza ufulu* kwa anthu onse okhala m’dzikolo.+ Chizikhala Chaka cha Ufulu+ kwa inu, ndipo aliyense wa inu azibwerera kumalo ake ndi kubanja lake.+
21 “Muzigwira ntchito zanu kwa masiku 6, koma pa tsiku la 7 muzisunga sabata.+ M’nyengo yolima ndi m’nyengo yokolola muzisunga sabata.+
4 Koma m’chaka cha 7 dzikolo lizisunga sabata lopuma pa zonse,+ sabata la Yehova. Musalime minda yanu, ndipo musatengulire mitengo yanu ya mpesa.
10 Chaka cha 50 chizikhala chopatulika, ndipo muzilengeza ufulu* kwa anthu onse okhala m’dzikolo.+ Chizikhala Chaka cha Ufulu+ kwa inu, ndipo aliyense wa inu azibwerera kumalo ake ndi kubanja lake.+