Deuteronomo 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “‘Posunga tsiku la sabata ndi kuliona kukhala lopatulika, mmene Yehova Mulungu wako anakulamulira,+ Mateyu 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pakuti Mwana wa munthu+ ndiye Mbuye wa sabata.”+ Luka 13:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma mtsogoleri wa sunagoge ataona izi, anakwiya chifukwa Yesu anachiritsa munthu pa sabata.+ Choncho anayamba kuuza khamu la anthu kuti: “Pali masiku 6 oyenera kugwira ntchito. Muzibwera masiku amenewo kudzachiritsidwa, osati tsiku la sabata.”+
12 “‘Posunga tsiku la sabata ndi kuliona kukhala lopatulika, mmene Yehova Mulungu wako anakulamulira,+
14 Koma mtsogoleri wa sunagoge ataona izi, anakwiya chifukwa Yesu anachiritsa munthu pa sabata.+ Choncho anayamba kuuza khamu la anthu kuti: “Pali masiku 6 oyenera kugwira ntchito. Muzibwera masiku amenewo kudzachiritsidwa, osati tsiku la sabata.”+