Ekisodo 20:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 muzichita ntchito zanu zonse masiku 6.+ Ekisodo 23:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Uzigwira ntchito masiku 6.+ Koma tsiku la 7 usamagwire ntchito, kuti ng’ombe yako ndi bulu wako zizipuma, ndipo mwana wa kapolo wako wamkazi ndi mlendo azipumula.+ Ekisodo 35:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Muzigwira ntchito masiku 6,+ koma tsiku la 7 likhale lopatulika kwa inu, likhale sabata la Yehova lopuma pa ntchito zanu zonse. Aliyense wogwira ntchito pa tsikuli adzaphedwa.+
12 “Uzigwira ntchito masiku 6.+ Koma tsiku la 7 usamagwire ntchito, kuti ng’ombe yako ndi bulu wako zizipuma, ndipo mwana wa kapolo wako wamkazi ndi mlendo azipumula.+
2 Muzigwira ntchito masiku 6,+ koma tsiku la 7 likhale lopatulika kwa inu, likhale sabata la Yehova lopuma pa ntchito zanu zonse. Aliyense wogwira ntchito pa tsikuli adzaphedwa.+