-
Levitiko 25:51Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
51 Ngati kwatsala zaka zochuluka, ndalama zake zodziwombolera zizigwirizana ndi zaka zimene zatsala, kuchotsera pa ndalama zimene anam’gulira.
-