-
Rute 4:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Ndiye ine ndaganiza zoti ndikuuze kuti, ‘Ugule mundawo+ pamaso pa anthu ndi pamaso pa akulu a mzinda uno.+ Ngati ukufuna kuuwombola, uwombole. Koma ngati sukufuna undiuze kuti ndidziwe, popeza palibenso wina amene angauwombole koma iweyo,+ pambuyo pako pali ine.’” Pamenepo, wowombola uja anati: “Ndiuwombola ineyo.”+
-
-
Rute 4:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Poyankha wowombolayo anati: “Sinditha kuuwombola, kuopera kuti ndingawononge cholowa changa. Iweyo uuwombole m’malo mwa ine, chifukwa ine sinditha kuuwombola.”
-