Genesis 23:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 pamaso pa ana a Heti ndi onse amene analowa pachipata cha mzinda, kuti Abulahamu ndiye wagula malowo ndipo ndi ake.+ Yeremiya 32:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndinalemba chikalata cha pangano+ ndi kuikapo chidindo,+ ndipo ndinaitana mboni+ kuti zidzasaine chikalatacho. Kenako ndinamuyezera+ ndalamazo pasikelo.
18 pamaso pa ana a Heti ndi onse amene analowa pachipata cha mzinda, kuti Abulahamu ndiye wagula malowo ndipo ndi ake.+
10 Ndinalemba chikalata cha pangano+ ndi kuikapo chidindo,+ ndipo ndinaitana mboni+ kuti zidzasaine chikalatacho. Kenako ndinamuyezera+ ndalamazo pasikelo.