-
Yeremiya 32:44Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
44 “‘Anthu adzagula minda ndi ndalama ndipo padzakhala kulemberana zikalata za pangano+ pamaso pa mboni ndi kumata zikalatazo.+ Zimenezi zidzachitika m’dziko la Benjamini,+ m’madera ozungulira Yerusalemu,+ m’mizinda ya Yuda,+ m’mizinda ya m’madera amapiri, m’mizinda ya m’chigwa+ ndi m’mizinda ya kum’mwera.+ Zidzakhala choncho chifukwa chakuti ndidzabwezeretsa anthu ake amene anagwidwa ndi kutengedwa kupita kudziko lina,’+ watero Yehova.”
-