Yeremiya 32:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndinalemba chikalata cha pangano+ ndi kuikapo chidindo,+ ndipo ndinaitana mboni+ kuti zidzasaine chikalatacho. Kenako ndinamuyezera+ ndalamazo pasikelo.
10 Ndinalemba chikalata cha pangano+ ndi kuikapo chidindo,+ ndipo ndinaitana mboni+ kuti zidzasaine chikalatacho. Kenako ndinamuyezera+ ndalamazo pasikelo.