Rute 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako Boazi anauza akulu ndi anthu onse kuti: “Inu ndinu mboni+ lero kuti ndikugula kwa Naomi zonse zimene zinali za Elimeleki, ndi zonse zimene zinali za Kiliyoni ndi Maloni. Yesaya 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndikufuna mboni zokhulupirika kuti zindichitire umboni.+ Mbonizo zikhale wansembe Uriya+ ndi Zekariya mwana wa Yeberekiya.”
9 Kenako Boazi anauza akulu ndi anthu onse kuti: “Inu ndinu mboni+ lero kuti ndikugula kwa Naomi zonse zimene zinali za Elimeleki, ndi zonse zimene zinali za Kiliyoni ndi Maloni.
2 Ndikufuna mboni zokhulupirika kuti zindichitire umboni.+ Mbonizo zikhale wansembe Uriya+ ndi Zekariya mwana wa Yeberekiya.”