Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 23:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 pamaso pa ana a Heti ndi onse amene analowa pachipata cha mzinda, kuti Abulahamu ndiye wagula malowo ndipo ndi ake.+

  • Deuteronomo 19:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 “Munthu akachita tchimo, mboni imodzi si yokwanira kutsimikizira kuti wachitadi cholakwacho kapena tchimo lililonse.+ Muzitsimikizira nkhaniyo mutamva umboni wapakamwa pa mboni ziwiri kapena zitatu.+

  • Rute 4:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ndiye ine ndaganiza zoti ndikuuze kuti, ‘Ugule mundawo+ pamaso pa anthu ndi pamaso pa akulu a mzinda uno.+ Ngati ukufuna kuuwombola, uwombole. Koma ngati sukufuna undiuze kuti ndidziwe, popeza palibenso wina amene angauwombole koma iweyo,+ pambuyo pako pali ine.’” Pamenepo, wowombola uja anati: “Ndiuwombola ineyo.”+

  • Yeremiya 32:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Kenako ndinapereka chikalata cha pangano chogulira mundawo kwa Baruki+ mwana wa Neriya+ mwana wa Maseya. Ndinamupatsa chikalata chimenechi pamaso pa Hanameli mwana wa m’bale wa bambo anga, pamaso pa mboni zimene zinasaina chikalatacho+ ndi pamaso pa Ayuda onse amene anali m’Bwalo la Alonda.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena