59 Mneneri Yeremiya anapereka malangizo kwa Seraya mwana wa Neriya+ mwana wa Maseya.+ Anapereka malangizowo pamene Seraya anapita ndi Zedekiya mfumu ya Yuda ku Babulo m’chaka chachinayi cha ufumu wake. Pa nthawiyo Seraya anali mkulu woyang’anira zinthu za mfumu.