Yeremiya 36:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno Yeremiya anaitana Baruki+ mwana wa Neriya kuti adzamuuze mawu onse amene Yehova anauza Yeremiyayo ndi kuti Baruki alembe mawuwo mumpukutu.+ Yeremiya 36:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Komanso mfumu inalamula Yerameeli mwana wa mfumu, Seraya mwana wa Azirieli ndi Selemiya mwana wa Abideeli kuti akagwire Baruki mlembi ndi mneneri Yeremiya,+ koma Yehova anawabisa.+
4 Ndiyeno Yeremiya anaitana Baruki+ mwana wa Neriya kuti adzamuuze mawu onse amene Yehova anauza Yeremiyayo ndi kuti Baruki alembe mawuwo mumpukutu.+
26 Komanso mfumu inalamula Yerameeli mwana wa mfumu, Seraya mwana wa Azirieli ndi Selemiya mwana wa Abideeli kuti akagwire Baruki mlembi ndi mneneri Yeremiya,+ koma Yehova anawabisa.+