1 Mafumu 17:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Choka kuno, lowera chakum’mawa ukabisale+ m’chigwa* cha Keriti, chimene chili kum’mawa kwa Yorodano. Yeremiya 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Iwo adzamenyana nawe ndithu, koma sadzapambana,+ pakuti Yehova wanena kuti, ‘Ine ndili ndi iwe+ kuti ndikulanditse.’”+ 2 Petulo 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chotero, zimenezi zikusonyeza kuti Yehova amadziwa kupulumutsa anthu odzipereka kwa iye akakhala pa mayesero.+ Koma anthu osalungama amawasungira tsiku loweruza kuti adzawawononge,+
3 “Choka kuno, lowera chakum’mawa ukabisale+ m’chigwa* cha Keriti, chimene chili kum’mawa kwa Yorodano.
19 Iwo adzamenyana nawe ndithu, koma sadzapambana,+ pakuti Yehova wanena kuti, ‘Ine ndili ndi iwe+ kuti ndikulanditse.’”+
9 Chotero, zimenezi zikusonyeza kuti Yehova amadziwa kupulumutsa anthu odzipereka kwa iye akakhala pa mayesero.+ Koma anthu osalungama amawasungira tsiku loweruza kuti adzawawononge,+