Salimo 31:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mudzawabisa m’malo otetezeka pafupi ndi inu,+Kuwachotsa pamaso pa anthu amene asonkhana pamodzi kuti awachitire chiwembu.+Mudzawabisa mumsasa wanu kwa anthu ofuna kukangana nawo.+ Salimo 83:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iwo amakumana mwachinsinsi kuti akambirane zochitira chiwembu anthu anu.+Ndipo amakonzera chiwembu anthu anu obisika.+
20 Mudzawabisa m’malo otetezeka pafupi ndi inu,+Kuwachotsa pamaso pa anthu amene asonkhana pamodzi kuti awachitire chiwembu.+Mudzawabisa mumsasa wanu kwa anthu ofuna kukangana nawo.+
3 Iwo amakumana mwachinsinsi kuti akambirane zochitira chiwembu anthu anu.+Ndipo amakonzera chiwembu anthu anu obisika.+