Yeremiya 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Ndisanakuumbe m’mimba,+ ndinakudziwa,+ ndipo usanatuluke m’mimbamo, ndinakusankha kuti uchite ntchito yopatulika.+ Ndinakusankha kuti ukhale mneneri ku mitundu ya anthu.” Mateyu 27:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamenepo zimene zinanenedwa kudzera mwa mneneri Yeremiya* zinakwaniritsidwa. Iye anati: “Ndipo anatenga ndalama 30 zasiliva,+ zomwe zinali mtengo wogulira munthu umene ena mwa ana a Isiraeli anamuikira,
5 “Ndisanakuumbe m’mimba,+ ndinakudziwa,+ ndipo usanatuluke m’mimbamo, ndinakusankha kuti uchite ntchito yopatulika.+ Ndinakusankha kuti ukhale mneneri ku mitundu ya anthu.”
9 Pamenepo zimene zinanenedwa kudzera mwa mneneri Yeremiya* zinakwaniritsidwa. Iye anati: “Ndipo anatenga ndalama 30 zasiliva,+ zomwe zinali mtengo wogulira munthu umene ena mwa ana a Isiraeli anamuikira,