Luka 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 chifukwa adzakhala wamkulu pamaso pa Yehova.+ Koma asadzamwe vinyo ngakhale pang’ono+ kapena chakumwa chaukali chilichonse. Ndipo adzadzazidwa ndi mzimu woyera kuyambira ali m’mimba mwa mayi ake.+
15 chifukwa adzakhala wamkulu pamaso pa Yehova.+ Koma asadzamwe vinyo ngakhale pang’ono+ kapena chakumwa chaukali chilichonse. Ndipo adzadzazidwa ndi mzimu woyera kuyambira ali m’mimba mwa mayi ake.+