Numeri 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 azisala vinyo ndi zakumwa zina zoledzeretsa.+ Asamamwe ngakhale viniga* wochokera ku vinyo, kapena viniga wochokera ku zakumwa zina zoledzeretsa, kapenanso madzi a mphesa. Ndiponso asamadye mphesa zaziwisi kapena zouma. Oweruza 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Choncho samala, usamwe vinyo kapena chakumwa chilichonse choledzeretsa,+ ndipo usadye chilichonse chodetsedwa.+ Mateyu 11:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mofanana ndi zimenezi, Yohane anabwera ndipo sanali kudya kapena kumwa.+ Koma anthu ankanena kuti, ‘Ali ndi chiwanda.’
3 azisala vinyo ndi zakumwa zina zoledzeretsa.+ Asamamwe ngakhale viniga* wochokera ku vinyo, kapena viniga wochokera ku zakumwa zina zoledzeretsa, kapenanso madzi a mphesa. Ndiponso asamadye mphesa zaziwisi kapena zouma.
4 Choncho samala, usamwe vinyo kapena chakumwa chilichonse choledzeretsa,+ ndipo usadye chilichonse chodetsedwa.+
18 Mofanana ndi zimenezi, Yohane anabwera ndipo sanali kudya kapena kumwa.+ Koma anthu ankanena kuti, ‘Ali ndi chiwanda.’