Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 10:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 “Pamene mukubwera kuchihema chokumanako, iwe ndi ana ako musamamwe vinyo kapena zakumwa zina zoledzeretsa,+ kuti mungafe. Limeneli ndi lamulo ku mibadwo yanu yonse mpaka kalekale,

  • Oweruza 13:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Asadye chilichonse chochokera ku mphesa zopangira vinyo, asamwe vinyo+ kapena chakumwa chilichonse choledzeretsa, ndipo asadye chilichonse chodetsedwa.+ Asunge zonse zimene ndamuuza.”+

  • Amosi 2:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 “‘Koma inu munapitiriza kupatsa Anaziri vinyo kuti amwe+ ndipo aneneri munawalamula kuti: “Musamanenere.”+

  • Luka 1:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 chifukwa adzakhala wamkulu pamaso pa Yehova.+ Koma asadzamwe vinyo ngakhale pang’ono+ kapena chakumwa chaukali chilichonse. Ndipo adzadzazidwa ndi mzimu woyera kuyambira ali m’mimba mwa mayi ake.+

  • Luka 7:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Mofanana ndi zimenezi, Yohane M’batizi anabwera ndipo sadya chakudya kapena kumwa vinyo, koma inu mumanena kuti, ‘Ali ndi chiwanda.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena