Yeremiya 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Ndisanakuumbe m’mimba,+ ndinakudziwa,+ ndipo usanatuluke m’mimbamo, ndinakusankha kuti uchite ntchito yopatulika.+ Ndinakusankha kuti ukhale mneneri ku mitundu ya anthu.” Aroma 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mapasawo asanabadwe ndiponso asanachite chilichonse chabwino kapena choipa,+ kuti cholinga cha Mulungu powasankha chikhalebe chodalira Iye amene amaitana,+ osati chodalira ntchito, Agalatiya 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma pamene Mulungu, amene anandichititsa kuti ndibadwe, anandiitana+ mwa kukoma mtima kwake kwakukulu,+ kunamukomera
5 “Ndisanakuumbe m’mimba,+ ndinakudziwa,+ ndipo usanatuluke m’mimbamo, ndinakusankha kuti uchite ntchito yopatulika.+ Ndinakusankha kuti ukhale mneneri ku mitundu ya anthu.”
11 Mapasawo asanabadwe ndiponso asanachite chilichonse chabwino kapena choipa,+ kuti cholinga cha Mulungu powasankha chikhalebe chodalira Iye amene amaitana,+ osati chodalira ntchito,
15 Koma pamene Mulungu, amene anandichititsa kuti ndibadwe, anandiitana+ mwa kukoma mtima kwake kwakukulu,+ kunamukomera