1 Akorinto 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Ine Paulo, woitanidwa kukhala mtumwi+ wa Yesu Khristu mwa chifuniro cha Mulungu,+ pamodzi ndi Sositene+ m’bale wathu, 1 Atesalonika 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 n’cholinga choti mupitirize kuyenda+ m’njira imene Mulungu, amene akukuitanani+ ku ufumu+ wake ndi ulemerero, amafuna.
1 Ine Paulo, woitanidwa kukhala mtumwi+ wa Yesu Khristu mwa chifuniro cha Mulungu,+ pamodzi ndi Sositene+ m’bale wathu,
12 n’cholinga choti mupitirize kuyenda+ m’njira imene Mulungu, amene akukuitanani+ ku ufumu+ wake ndi ulemerero, amafuna.