2 Akorinto 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Ine Paulo, mtumwi+ wa Khristu Yesu mwa kufuna kwa Mulungu, ndikulembera mpingo wa Mulungu wa ku Korinto, pamodzi ndi oyera onse+ amene ali mu Akaya+ monse, ndili limodzi ndi Timoteyo+ m’bale wathu, kuti: Akolose 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Ine Paulo, mtumwi wa Khristu Yesu mwa kufuna kwa Mulungu,+ pamene ndili limodzi ndi Timoteyo+ m’bale wathu,
1 Ine Paulo, mtumwi+ wa Khristu Yesu mwa kufuna kwa Mulungu, ndikulembera mpingo wa Mulungu wa ku Korinto, pamodzi ndi oyera onse+ amene ali mu Akaya+ monse, ndili limodzi ndi Timoteyo+ m’bale wathu, kuti:
1 Ine Paulo, mtumwi wa Khristu Yesu mwa kufuna kwa Mulungu,+ pamene ndili limodzi ndi Timoteyo+ m’bale wathu,