Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 13:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Pakuti udzatenga pakati ndi kubereka mwana wamwamuna. M’mutu mwake musadzadutse lezala+ chifukwa mwanayo adzakhala Mnaziri+ wa Mulungu potuluka m’mimba.+ Iye adzakhala patsogolo populumutsa Isiraeli m’manja mwa Afilisiti.”+

  • Yesaya 45:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 45 Ine Yehova ndalankhula kwa wodzozedwa wanga.+ Ndalankhula kwa Koresi amene ndamugwira dzanja lake lamanja+ kuti ndigonjetse mitundu ya anthu pamaso pake,+ kuti ndimasule m’chiuno mwa mafumu, kuti ndimutsegulire zitseko zokhala ziwiriziwiri, moti ngakhale zipata sizidzatsekedwa. Ndalankhula kuti:

  • Aroma 9:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Mapasawo asanabadwe ndiponso asanachite chilichonse chabwino kapena choipa,+ kuti cholinga cha Mulungu powasankha chikhalebe chodalira Iye amene amaitana,+ osati chodalira ntchito,

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena