Rute 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Gona pompano lero. Ngati iye angakuwombole+ mawa, zili bwino! Akuwombole. Koma ngati sakufuna kukuwombola, ineyo ndidzakuwombola. Ndithudi, pali Yehova Mulungu wamoyo,+ ndidzakuwombola. Gona kufikira m’mawa.”
13 Gona pompano lero. Ngati iye angakuwombole+ mawa, zili bwino! Akuwombole. Koma ngati sakufuna kukuwombola, ineyo ndidzakuwombola. Ndithudi, pali Yehova Mulungu wamoyo,+ ndidzakuwombola. Gona kufikira m’mawa.”