Rute 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamenepo anafunsa kuti: “Ndiwe yani?” Poyankha, Rute anati: “Ndine Rute kapolo wanu. Mufunditse kapolo wanu chovala chanu, pakuti ndinu wotiwombola.”+ Rute 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako Boazi anati: “Ukadzagula mundawo kwa Naomi, ndiye kuti waugulanso kwa Rute Mmowabu, amene mwamuna wake anamwalira, kuti dzina la mwamuna wakeyo libwerere pacholowa chake.”+ Mateyu 22:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 “Mphunzitsi, Mose anati, ‘Ngati munthu wamwalira wopanda ana, m’bale wake ayenera kukwatira mkazi wamasiyeyo ndi kuberekera m’bale wake uja ana.’+
9 Pamenepo anafunsa kuti: “Ndiwe yani?” Poyankha, Rute anati: “Ndine Rute kapolo wanu. Mufunditse kapolo wanu chovala chanu, pakuti ndinu wotiwombola.”+
5 Kenako Boazi anati: “Ukadzagula mundawo kwa Naomi, ndiye kuti waugulanso kwa Rute Mmowabu, amene mwamuna wake anamwalira, kuti dzina la mwamuna wakeyo libwerere pacholowa chake.”+
24 “Mphunzitsi, Mose anati, ‘Ngati munthu wamwalira wopanda ana, m’bale wake ayenera kukwatira mkazi wamasiyeyo ndi kuberekera m’bale wake uja ana.’+