-
Ezekieli 45:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Muyezo wa efa ndi wa mtsuko woyezera uzikhala wofanana komanso wosasinthasintha. Muyezo wa mtsuko uzikhala wokwanira gawo limodzi mwa magawo 10 a homeri.* Gawo limodzi mwa magawo 10 la muyezo wa homeri lizifanana ndi muyezo wa efa.+ Muzipeza miyezo yoyenera ya zimenezi potengera muyezo wa nthawi zonse wa homeri.
-