Yakobo 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma lilime, palibe munthu ndi mmodzi yemwe angathe kuliweta. Ndilo kanthu kamodzi kosalamulirika ndi kovulaza, kodzaza ndi poizoni wakupha.+ 1 Petulo 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti “amene akufuna kusangalala ndi moyo ndi kuona masiku abwino,+ aletse lilime+ lake kuti lisalankhule zoipa ndi milomo yake kuti isalankhule chinyengo,+
8 Koma lilime, palibe munthu ndi mmodzi yemwe angathe kuliweta. Ndilo kanthu kamodzi kosalamulirika ndi kovulaza, kodzaza ndi poizoni wakupha.+
10 Pakuti “amene akufuna kusangalala ndi moyo ndi kuona masiku abwino,+ aletse lilime+ lake kuti lisalankhule zoipa ndi milomo yake kuti isalankhule chinyengo,+