Levitiko 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 kapena chilichonse chimene angalumbirire monama. Azibweza+ chinthucho ndi kuwonjezerapo limodzi mwa magawo ake asanu. Iye azibweza zimenezi kwa mwiniwake, tsiku limene kulakwa kwake kwatsimikizidwa. Levitiko 22:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “‘Munthu akadya mosadziwa chinthu chopatulika,+ azibwezera chinthucho ndi kuwonjezerapo gawo limodzi mwa magawo ake asanu.+ Azipereka chinthu chopatulikacho kwa wansembe. Levitiko 27:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma ngati akufuna kuiwombola, azipereka mtengo woikidwiratu wa nyamayo ndi kuwonjezerapo limodzi mwa magawo asanu+ a mtengowo. Numeri 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Munthuyo aziulula+ tchimo lake limene wachita. Azipereka malipiro onse a mlandu wake, komanso aziwonjezerapo limodzi mwa magawo asanu a malipirowo.+ Azipereka malipirowo kwa munthu amene wam’lakwira.
5 kapena chilichonse chimene angalumbirire monama. Azibweza+ chinthucho ndi kuwonjezerapo limodzi mwa magawo ake asanu. Iye azibweza zimenezi kwa mwiniwake, tsiku limene kulakwa kwake kwatsimikizidwa.
14 “‘Munthu akadya mosadziwa chinthu chopatulika,+ azibwezera chinthucho ndi kuwonjezerapo gawo limodzi mwa magawo ake asanu.+ Azipereka chinthu chopatulikacho kwa wansembe.
13 Koma ngati akufuna kuiwombola, azipereka mtengo woikidwiratu wa nyamayo ndi kuwonjezerapo limodzi mwa magawo asanu+ a mtengowo.
7 Munthuyo aziulula+ tchimo lake limene wachita. Azipereka malipiro onse a mlandu wake, komanso aziwonjezerapo limodzi mwa magawo asanu a malipirowo.+ Azipereka malipirowo kwa munthu amene wam’lakwira.